Welcome to Polymed Sacco
Polymed SaccoPolymed SaccoPolymed Sacco
(Monday - Saturday)
Chipatala Avenue, Near Beit Cure/DHO

Chidziwitso Cha Kalondolondo Wa Ma Mamembala

Kwa Ma Membala Onse a Polymed Sacco

CHIDZIWITSO CHA KALONDOLONDO WA MA MAMEMBALA

Ma membala Onse a Polymed Sacco akudziwitsidwa kuti akuyenela kupeleka zonse zofunikila pa kalondolondo wa ma membala a Sacco pasanafike pa 15 August 2024

 

Zofunikila Kudziwa

Ndi anthu ati amene akuyenela kupeleka zofunikila?

  • Ma Membala onse a Polymed Sacco

Zofunika ndi chani?

Zonse Zofunika pa ndondomekoyi monga kujambulidwa chithunzi cha nkhope, chitupa chanu cha unzika (Kumaso ndi kumbuyo).

Katumizidwe ka zofunikila

  • Pa makina a whatsapp nambala iyi +265885512108
  • Ku ma office athu ku Blantyre ndi ku Lilongwe

Kufunika kwake ndikotani?

Kupeleka zikalata ndikofunika pa zifukwa izi:

  • Kuthandiza kuonetsetsa kuti Sacco ikhale ndi mafailo olondola a ma membala ake
  • Kukwanilitsa zofunika pa malamulo a boma
  • Kuthandiza kupititsa patsogolo ntchito za Sacco komaso kufalitsa ma uthenga

Chidziwitso: Tiyeni tichitenge chofunikila kupanga nawo ndondomekoyi kuopa chisokoneko chilichonse chomwe chingabwele pakunyozela.

Zikomo

POLYMED SACCO LTD

Polymed Sacco

Chipatala Avenue, Near Beit Cure/DHO, Blantyre.
+265 998 300 203
(08:00am - 03:30 pm)